Young Adult [YA] Fiction
DZIWANI ZAMATENDA OTHAMANGA MAGAZI
Author
Henry Ndhlovu
Description
Bukhuli lalembedwa pongochotsa ndime ina mubuku langa lotchedwa " *Turning Dreams Into Reality: Fighting Hypertension in Low-Resource Settings of Malawi through Moyowathu HealthCare Services".*
Izi zachitika kutsatira pempho laena kuti ndiike padera ndime imeneyi ndipo ndikukhulupilira likhala laphindu kwaonse oliwelenga.
Ambiri tikudziwa mavuto omwe amadza chifukwa chamatenda othamanga magazi ndiye iyi ndimbali ina yothandizila kulimbana ndimatendawa.
Kuchokera mundondomekoyi titha kulumikizana ndipo ngati nkotheka kuyezana BP ndikupatsana uphungu.