Atumiki mu Utumiki
Autobiography

Atumiki mu Utumiki

Author

Lindelwa Topham Thole

Description

Buku ili Atumiki mu Utumiki, linamasulidwa kuchokela mu buku la chizungu lomwe ndinalemba lotchedwa ministers in the ministry.  Atumiki mu Utumiki kutanthauza atsogoleri a mpingo Abusa.  Atumikiwa, Abusa anayitanidwa ndi Mulungu ndi kupatsidwa ntchito ndi Mulungu kuti akayigwira momwe mmene Mulungu anayiperekela. Kodi ndi Abusa onse amene akutumikiladi moyenera? Pezani yankho mu buku ili

Share this book

Share this book with friends and family