Autobiography
KUKHUZA KWA MKAZI WA MBUSA
Author
Lindelwa Topham Thole
Description
Bukuli linamasulidwa kuchokela mu buku langa loyamba lomwe ndinalemba lotchedwa Influence of Pastor's wives. Bukuli linabwera ndi funso lodabwitsa loti "Kodi ukudziwa kuti amayi busa ambiri kumapeto kwa nyengo adzalephera kulowa ufumu wa Mulungu" Ndinadabwa kuti funsoli likubwera bwanji? Ndipo likutanthauza chani. Koma pakhalekhale ndipamene Mzimu Woyera anayamba kuvumbulutsa Mau a mubukuli. Amayi busa, akazi a atsogoleri mu mpingo ndi maudindo osiyanasiyana komanso atsogoleri achizimayi werengani Bukuli kuti muphunzire ndi kusamalira utumiki kapena ntchito yanu
...